‘Chiwerewere chakula kwambiri ku Mwanza, Abambo ambiri ikuyenda m’manja’
Mfumu yaikulu Nthache ya m’boma la Mwanza yati m’chitidwe wa chiwerewere pakati pa atsikana oyendayenda, ena mwa anthu oyedetsa galimoto onyamula katundu komanso anthu ochita malonda pakati pa dziko lino ndi maiko ena kudzera ku chipata cha Mwanza wakula kwambiri. Mfumu Nthache yati kukhalitsa kwa anthu ochita malonda pa chipata cha Mwanza pamene akufuna kuombola […]
Читать дальше...