Мы в Telegram
Добавить новость
ru24.net
News in English
Декабрь
2022

A Mutharika akulingalira zozapikisana nawo pa chisankho chamu 2025

0

Mtsogoleri wa chipani cha Democratic Progressive (DPP) Professor Peter Mutharika wati akulingalira ngati azapikisane nawo pa chisankho cha mtsogoleri wa dziko lino m’chaka cha 2025. A Mutharika anena izi pa msonkhano wa ndale omwe anachititsa Loweruka pa bwalo la masewero apa St Augustine 3 Primary School m’boma la Mangochi. Iwo ati anthu ochuluka akuwafunsa kuti […]

The post A Mutharika akulingalira zozapikisana nawo pa chisankho chamu 2025 appeared first on Malawi Voice.

Mtsogoleri wa chipani cha Democratic Progressive (DPP) Professor Peter Mutharika wati akulingalira ngati azapikisane nawo pa chisankho cha mtsogoleri wa dziko lino m’chaka cha 2025.

A Mutharika anena izi pa msonkhano wa ndale omwe anachititsa Loweruka pa bwalo la masewero apa St Augustine 3 Primary School m’boma la Mangochi.

Iwo ati anthu ochuluka akuwafunsa kuti apikitsane nawo pa chisankho m’chaka cha 2025 ngati mtsogoleri wa dziko lino.

Apa a Mutharika ati akukhulupilira kuti chipani cha DPP chibweleranso m’boma posachedwapa kaamba koti Mgwirizano wa Tonse walephera.

Iwo ati chipani cha DPP mulibe kugawanika koma muli Mgwirizano ndipo anthu apitilire kusatila chipanichi.

Pa msonkhanowu panali anthu omwe aonetsa chidwi chopikitsana pa mpando wa mtsogoleri wa chipani cha DPP monga Dr. Kondwani Nankhumwa, Bright Msaka, Joseph Mwanamveka, George Chaponda mwa ena.

The post A Mutharika akulingalira zozapikisana nawo pa chisankho chamu 2025 appeared first on Malawi Voice.




Moscow.media
Частные объявления сегодня





Rss.plus




Спорт в России и мире

Новости спорта


Новости тенниса
Анна Блинкова

Россиянки Аванесян и Блинкова вышли во второй тур турнира в Риме






Московские прогулки, ч.21

Девочка упала в строительную шахту и скончалась на западе Москвы

SHOT: склад с поликарбонатом загорелся в подмосковном Наро-Фоминске

Школьница насмерть разбилась после падения в шахту заброшенного дома в Москве