Mtsogoleri wakale wa dziko lino a Peter Mutharika ati akukhulupilira kuti a Malawi anachita kupepetulidwa kuti avotere a Lazarus Chakwera pa chisankho cha m’chaka cha 2020. A Mutharika, omwenso ndi mtsogoleri wa chipani cha DPP, amayakhula izi Lachisanu m’boma la Mangochi. M’mawu aw, a Mutharika anati kaamba ka kusamva, a Malawi anasankha mtsogoleri yemwe pakadali […]
Mtsogoleri wakale wa dziko lino a Peter Mutharika ati akukhulupilira kuti a Malawi anachita kupepetulidwa kuti avotere a Lazarus Chakwera pa chisankho cha m’chaka cha 2020.
A Mutharika, omwenso ndi mtsogoleri wa chipani cha DPP, amayakhula izi Lachisanu m’boma la Mangochi.
M’mawu aw, a Mutharika anati kaamba ka kusamva, a Malawi anasankha mtsogoleri yemwe pakadali pano akulephera kuyendetsa bwino chuma cha dziko lino.
Iwo anati adalangiza kangapo konse a Malawi kuti akasankha boma lilipoli ndiye kuti asankha mavuto koma iwo m’malo mwake anatukwanidwa kuti ndi okalamba.
“A Malawi kusamva, kaya kaya munalozedwa kaya ndi chani?…koma ndinakuchenjezani kangapo konse kuti musavotere MCP, koma inu mumandinena ine kuti ndine okalamba komanso opanda mano m’kamwa,” anatero a Mutharika
Malingana ndi a Mutharika chifukwa chosowa masophwenya boma la Chakwera lalephera kupeza ndondomeko zotuluka chuma cha dziko lino.
Pomaliza a Mutharika anati akukhulupilira kuti a Malawi tsopano aphunzirapo ndipo sazachitanso chibwana kuvotera MCP.
England U20 overpower France to be crowned world champions
Faculty of International Journalism and Mass Communications Eurasian International University is conducting an additional intake of applicants!
Exclusive - Sayantani Ghosh expresses happiness as sets of her show Dahej Daasi shifted close to her home; says 'I've been manifesting this for quite some time now'
Biden's anger bleeds through as party weighs his future
CD Projekt's Pawel Sasko tells the inspiring tale of how an Estonian beet farmer in Australia became a senior quest designer on The Witcher 4
D&D's new 2024 Player's Handbook will have 10 species to choose from including goliaths, and drow will be closer to their Baldur's Gate 3 version
Двадцать пять человек за одним столом под звуки караоке – это было шедеврально!
According to BioWare, Dragon Age: The Veilguard is the first entry in the series where "the combat's actually fun" and where characters are "intentionally" the focus of the storytelling, which seems pretty unfair on the first three games
Лоза раскрыл причины открытых комментариев на своих страницах в соцсетях
Гроссмейстер из Бурятии Жамсаран Цыдыпов продолжает лидировать на турнире «Moscow Open – 2024», набрав 6,5 очков после 7 туров, на пол-очка отстают Борис Савченко, Сергей Волков и Владимир Захарцов
Продвижение Музыки. Раскрутка Музыки. Продвижение Песни. Раскрутка Песни.
Элджей спровоцировал слухи о романе с известной певицей